Jeremiah 26:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komabe mfumu Yehoyakimu adatuma Elinatani mwana wa Akibori, pamodzi ndi anthu ena, ku Ejipito.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo Yehoyakimu mfumu anatuma anthu ku Ejipito, Elinatani mwana wake wa Akibori, ndi anthu ena pamodzi ndi iye, anke ku Ejipito;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Komabe Mfumu Yehoyakimu anatuma Elinatani mwana wa Akibori pamodzi ndi anthu ena, ku Igupto.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo Yehoyakimu mfumu anatuma anthu ku Aigupto, Elinatanu mwana wace wa Akibori, ndi anthu ena pamodzi ndi iye, anke ku Aigupto;