Jeremiah 27:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene Zedekiya, mwana wa Yosiya mfumu ya ku Yuda adayamba kulamulira, Chauta adalankhula ndi Yeremiya namuuza kuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Poyamba kukhala mfumu Yehoyakimu mwana wake wa Yosiya, mfumu ya Yuda, mau awa anadza kwa Yeremiya kuchokera kwa Yehova, kuti,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zedekiya mwana wa Yosiya, mfumu ya ku Yuda, atangoyamba kulamulira, Yehova anawuza Yeremiya kuti,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Poyamba kukhala mfumu Yehoyakimu mwana wace wa Yosiya, mfumu ya Yuda, mau awa anadza kwa Yeremiya kucokera kwa Yehova, kuti,