Jeremiah 27:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndithudi, amakuloserani zabodza, kotero kuti adani adzakuchotsani m'dziko lanu, kupita nanu kutali. Ndidzakupirikitsani ndipo mudzaonongeka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kakuti iwo akunenerani inu zonama, kuti akuchotseni inu m'dziko lanu, kunka kutali kuti ndikupirikitseni inu, ndipo inu mudzathedwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo akukuloserani zabodza kotero kuti adani adzakuchotsani mʼdziko lanu nʼkupita nanu ku dziko lakutali. Ndidzakupirikitsani ndi kukuwonongani kotheratu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kakuti iwo akunenerani inu zonama, kuti akucotseni inu m'dziko lanu, kunka kutari kuti ndikupitikitseni inu, ndipo inu mudzathedwa.