Jeremiah 27:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nanga iweyo ndi anthu ako, muferenji ndi nkhondo, njala ndi mliri, zimene Chauta waopsera mtundu wina uliwonse wosatumikira mfumu ya ku Babiloni?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mudzaferanji, iwe ndi anthu anu, ndi lupanga ndi njala, ndi chaola, monga wanena Yehova za mtundu umene ukana kumtumikira mfumu ya ku Babiloni?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nanga inu ndi anthu anu, muferenji ndi lupanga, ndi njala, ndi mliri, zimene Yehova waopsezera mtundu wina uliwonse umene sudzatumikira mfumu ya ku Babuloni?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mudzaferanji, iwe ndi anthu anu, ndi lupanga ndi njala, ndi caola, monga wanena Yehova za mtundu umene ukana kumtumikira mfumu ya ku Babulo?