Jeremiah 27:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zoonadi, ameneŵa ndiwo mau a Chauta Wamphamvuzonse onena za ziŵiya zimene zidatsala m'Nyumba ya Chauta, m'nyumba ya mfumu ya ku Yuda ndiponso mu Yerusalemu, akuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
inde, atero Yehova wa makamu, Mulungu wa Israele, za zipangizo zotsala m'nyumba ya Yehova, ndi m'nyumba ya mfumu ya Yuda, ndi ku Yerusalemu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inde, Yehova Wamphamvuzonse, Mulungu wa Israeli, akunena za zinthu zimene zinatsala mʼNyumba ya Yehova ndi mʼnyumba ya mfumu ya Yuda ndi mu Yerusalemu kuti,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
inde, atero Yehova, Mulungu wa Israyeli, za zipangizo zotsala m'nyumba ya Yehova, ndi m'nyumba ya mfumu ya Yuda, ndi ku Yerusalemu;