Jeremiah 27:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono utumize uthenga kwa mafumu a ku Edomu, Mowabu, Amoni, Tiro ndi Sidoni, kudzera mwa amithenga amene abwera ku Yerusalemu kwa Zedekiya, mfumu ya ku Yuda.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nuzitumize kwa mfumu ya Edomu, ndi kwa mfumu ya Mowabu, ndi kwa mfumu ya ana a Amoni, ndi kwa mfumu ya Tiro, ndi kwa mfumu ya Sidoni, ndi dzanja la amithenga amene afika ku Yerusalemu kwa Zedekiya mfumu ya Yuda;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono utumize uthenga kwa mafumu a Edomu, Mowabu, Amoni, Turo ndi Sidoni kudzera mwa amithenga amene abwera ku Yerusalemu kwa Zedekiya, mfumu ya Yuda.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nuzitumize kwa mfumu ya Edomu, ndi kwa mfumu ya Moabu, ndi kwa mfumu ya ana a Amoni, ndi kwa mfumu ya Turo, ndi kwa mfumu ya Zidoni, ndi dzanja la amithenga amene afika ku Yerusalemu kwa Zedekiya mfumu ya Yuda;