Jeremiah 28:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Patapita nthaŵi pang'ono Hananiya atathyola goli m'khosi mwa Yeremiya, Chauta adauza Yeremiya kuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mau a Yehova anadza kwa Yeremiya, atathyola Hananiya mneneri goli kulichotsa pa khosi la Yeremiya, kuti,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Patapita nthawi pangʼono, mneneri Hananiya atathyola goli mʼkhosi mwa mneneri Yeremiya, Yehova anawuza Yeremiya kuti,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mau a Yehova anadza kwa Yeremiya, atatyola Hananiya mneneri gori kulicotsa pa khosi la Yeremiya, kuti,