Jeremiah 28:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Pita ukamuuze Hananiya mau a Chauta akuti, ‘Iweyo wathyola goli lamtengo, m'malo mwake Ine ndidzaika goli lachitsulo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pita, nunene kwa Hananiya, kuti Yehova atero: Wathyola magoli amtengo; koma udzapanga m'malo mwao magoli achitsulo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Pita, kawuze mneneri Hananiya kuti, ‘Yehova akuti: Iwe wathyola goli lamtengo, mʼmalo mwake Ine ndidzayika goli lachitsulo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pita, nunene kwa Hananiya, kuti Yehova atero: Watyola magori amtengo; koma udzapanga m'malo mwao magori acitsulo.