Jeremiah 28:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komabe ungomva zimene nditi ndikuuze iweyo ndi anthu onse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma mumvetu mau awa amene ndinena m'makutu anu, ndi m'makutu a anthu onse:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Komabe, tamvera zimene nditi ndikuwuze iweyo pamodzi ndi anthu onse:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma mumvetu mau awa amene ndinena m'makutu anu, ndi m'makutu a anthu onse: