Jeremiah 29:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu mumanena kuti, “Chauta adatipatsa aneneri athu ku Babiloni.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti mwati, Yehova watiutsira ife aneneri m'Babiloni.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu mumati, “Yehova watiwutsira aneneri athu ku Babuloni,”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti mwati, Yehova watiutsira ife aneneri m'Babulo.