Jeremiah 29:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Chauta alipo ndi mau pa za mfumu imene ikukhala pa mpando waufumu wa Davide, ndi pa za anthu onse okhala mu mzinda uno, ndiye kuti anzanu a m'dzikomo amene sadatengedwe nao ukapolo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti Yehova atero za mfumu imene ikhala pa mpando wachifumu wa Davide, ndi za anthu onse amene akhala m'mudzi uno, abale anu amene sanatulukire pamodzi ndi inu kundende;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
koma zimene Yehova akunena za mfumu imene ikukhala pa mpando waufumu wa Davide pamodzi ndi anthu onse amene anatsala mu mzinda muno, abale anu amene sanapite nanu ku ukapolo ndi izi,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti Yehova atero za mfumu imene ikhala pa mpando wacifumu wa Davide, ndi za anthu onse amene akhala m'mudzi uno, abale anu amene sanaturukira pamodzi ndiinu kundende;