Jeremiah 29:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akunena kuti, “Ndidzaŵapha ndi nkhondo, njala ndi mliri. Ndidzaŵasandutsa ngati nkhuyu zoola kwambiri, zosatinso nkudyeka ai.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova wa makamu atero: Taonani, ndidzatuma pa iwo lupanga, ndi njala, ndi chaola, ndipo ndidzayesa iwo onga nkhuyu zoola, zosadyeka, pokhala nzoipa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova Wamphamvuzonse akuti, “Ndidzawapha ndi nkhondo, njala ndi mliri ndipo ndidzawasandutsa ngati nkhuyu zowola kwambiri, zosati nʼkudya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova wa makamu atero: Taonani, ndidzatuma pa iwo lupanga, ndi njala, ndi caola, ndipo ndidzayesa iwo onga nkhuyu zoola, zosadyeka, pokhala nzoipa.