Jeremiah 29:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Izi zidzatero chifukwa sadamvere mau anga, pamene Ine ndidakhala ndikuŵatumizira aneneri, atumiki anga. Koma inunso simudamvere,” akuterotu Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
chifukwa sanamvere mau anga, ati Yehova, amene ndinawatumizira ndi atumiki anga aneneri, ndi kuuka mamawa ndi kuwatuma, koma munakana kumva, ati Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zidzatero chifukwa sanamvere mawu anga amene ndinkawatumizira kudzera mwa atumiki anga, aneneri. Ngakhale inu amene muli ku ukapolo simunamverenso,” akutero Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
cifukwa sanamvera mau anga, ati Yehova, amene ndinawatumizira ndi atumiki anga aneneri, ndi kuuka mamawa ndi kuwatuma, koma munakana kumva, ati Yehova.