Jeremiah 29:31 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Utume uthenga kwa akapolo onse, uŵauze mau a Chauta onena za Semaya wa ku Nehelamu, akuti, Semaya wakuloserani, ngakhale sindidamtume, ndipo wakunyengani kuti muzikhulupirira zabodza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Uwatumizire mau am'nsinga onse, akuti, Atero Yehova za Semaya Mnehelamu: Chifukwa Semaya wanenera kwa inu, koma Ine sindinamtuma, ndipo anakukhulupiritsani zonama;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Tumiza uthenga uwu kwa akapolo onse: ‘Yehova akuti zokhudza Semaya wa ku Nehelamu: Semaya wakuloserani, ngakhale kuti Ine sindinamutume, ndipo wakunyengani kuti muzikhulupirira bodza.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Uwatumizire mau am'nsinga onse, akuti, Atero Yehova za Semaya Mnehelamu: Cifukwa Semaya wanenera kwa inu, koma Ine sindinamtuma, ndipo anakukhulupiritsani zonama;