Jeremiah 29:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Anthu onse a ku Yerusalemu, amene adatengedwa ukapolo kupita ku Babiloni, Chauta Wamphamvuzonse, Mulungu wa Israele, akuŵauza kuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova wa makamu, Mulungu wa Israele atero, kwa am'nsinga onse, amene ndinawatenga ndende ku Yerusalemu kunka nao ku Babiloni:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu onse amene anatengedwa ukapolo kuchokera ku Yerusalemu kupita ku Babuloni, Yehova akuwawuza kuti,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova wa makamu, Mulungu wa Israyeli atero, kwa am'nsinga onse, amene ndinawatenga ndende ku Yerusalemu kunka nao ku Babulo: