Jeremiah 29:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndithu amakuloserani zabodza m'dzina langa, Ine sindidaŵatume,’ ” akutero Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti anenera kwa inu zonama m'dzina langa; sindinatuma iwo, ati Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo akunenera zabodza kwa inu mʼdzina langa ngakhale Ine sindinawatume,” akutero Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti anenera kwa inu zonama m'dzina langa; sindinatuma iwo, ati Yehova.