Jeremiah 3:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndithu, monga momwe mkazi wosakhulupirika amasiyira mwamuna wake, iwenso Israele wakhala wosakhulupirika kwa Ine,” akuterotu Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndithu monga mkazi achokera mwamuna wake monyenga, chomwecho mwachita ndi Ine monyenga, inu nyumba ya Israele, ati Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma monga mkazi wosakhulupirika amasiya mwamuna wake, momwemonso inu mwakhala osakhulupirika kwa Ine, inu fuko la Israeli,” akutero Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndithu monga mkazi acokera mwamuna wace monyenga, comweco mwacita ndi Ine monyenga, inu nyumba ya Israyeli, ati Yehova.