Jeremiah 3:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakumveka liwu pa magomo, Aisraele akulira ndiponso akupempha chifundo, pakuti atsata njira zoipa, ndipo aiŵala Chauta, Mulungu wao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mau amveka pa mapiri oti see, kulira ndi kupempha kwa ana a Israele; pakuti anaipitsa njira yao, naiwala Yehova Mulungu wao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mawu akumveka pa magomo, Aisraeli akulira ndi kupempha chifundo chifukwa anatsata njira zoyipa ndi kuyiwala Yehova Mulungu wawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mau amveka pa mapiri oti se, kulira ndi kupempha kwa ana a Israyeli; pakuti anaipitsa njira yao, naiwala Yehova Mulungu wao.