Jeremiah 3:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi si tsopano apa wakhala ukundiwuza kuti, ‘Atate, ndinu bwenzi la unyamata wanga,’ numadzifunsa kuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kodi kuyambira tsopano sudzafuulira kwa Ine, Atate wanga, wotsogolera ubwana wanga ndinu?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi iwe siposachedwa pomwepa pamene wanena kuti, ‘Abambo anga, Inu bwenzi langa la unyamata wanga,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kodi kuyambira tsopano sudzapfuulira kwa Ine, Atate wanga, wotsogolera ubwana wanga ndinu?