Jeremiah 30:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta akunena kuti, “Chilonda chanu nchosachizika, bala lanu nlonyeka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti atero Yehova, Kulaswa kwako kuli kosapoleka ndi bala lako lili lowawa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova akuti, “Chilonda chanu nʼchosachizika, bala lanu ndi lonyeka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti atero Yehova, Kulaswa kwako kuti kosapoleka ndi bala lako liri lowawa.