Jeremiah 30:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mkwiyo wa Chauta sudzachoka mpaka utatsiriza kuchita zonse zimene mtima wa Chautayo ukufuna. Mudzamvetsa zimenezi masiku akubwerawo.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mkwiyo waukali wa Yehova sudzabwerera, mpaka wachita, mpaka watha zomwe afuna kuchita m'mtima mwake: masiku akumaliza mudzachizindikira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mkwiyo woopsa wa Yehova sudzachoka mpaka atakwaniritsa zolinga za mu mtima mwake. Mudzamvetsa zimenezi masiku akubwerawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mkwiyo waukali wa Yehova sudzabwerera, mpaka wacita, mpaka watha zomwe afuna kucita m'mtima mwace: masiku akumariza mudzacizindikira.