Jeremiah 31:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta akunena kuti, “Pa nthaŵi imeneyo ndidzakhala Mulungu wa mabanja onse a Israele, ndipo iwo adzakhala anthu anga.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nthawi yomweyo, ati Yehova, ndidzakhala Mulungu wa mabanja onse a Israele, ndipo iwo adzakhala anthu anga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Pa nthawi imeneyo,” akutero Yehova, “Ndidzakhala Mulungu wa mafuko onse a Israeli, ndipo iwo adzakhala anthu anga.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nthawi yomweyo, ati Yehova, ndidzakhala Mulungu wa mabanja onse a Israyeli, ndipo iwo adzakhala anthu anga.