Jeremiah 31:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mau a Chauta ndi aŵa, “Anthu amene adapulumuka ku nkhondo, ndidaŵakomera mtima m'chipululu. Pamene Aisraele ankafuna kupumula,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Atero Yehova, Anthu opulumuka m'lupanga anapeza chisomo m'chipululu; Israele, muja anakapuma.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova akuti, “Anthu amene anapulumuka ku nkhondo ndinawakomera mtima mʼchipululu; pamene Aisraeli ankafuna kupumula.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Atero Yehova, Anthu opulumuka m'lupanga anapeza cisomo m'cipululu; Israyeli, muja anakapuma.