Jeremiah 31:27 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta akunena kuti, “Ikubwera nthaŵi pamene ndidzachulukitsa anthu ndi ziŵeto mu Israele ndi Yuda.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Taonani, masiku adza, ati Yehova, amene ndidzafesera nyumba ya Israele ndi nyumba ya Yuda ndi mbeu ya anthu ndi mbeu ya nyama.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Masiku akubwera,” akutero Yehova, “pamene ndidzachulukitsa anthu pamodzi ndi ziweto mʼdziko la Israeli ndi la Yuda.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Taonani, masiku adza, ati Yehova, amene ndidzafesera nyumba ya Israyeli ndi nyumba ya Yuda ndi mbeu ya anthu ndi mbeu ya nyama.