Jeremiah 31:28 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Monga momwe ndidaŵasamalira, kuŵazula, kuŵapasula, kuŵagumula, kuŵaononga ndi kuŵachita zoipa, momwemonso ndidzasamala kuti ndiŵamange ndi kuŵabzalanso,” akuterotu Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo padzakhala kuti, monga ndayang'anira iwo kuzula ndi kupasula ndi kugwetsa, ndi kuononga ndi kusautsa; momwemo ndidzayang'anira iwo kumangitsa mudzi ndi kubzala, ati Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Monga momwe ndinasamalira powazula, powagwetsa, powagumula, powawononga ndi powachita zoyipa, momwemonso ndidzasamala powamanga ndi powadzala” akutero Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo padzakhala kuti, monga ndayang'anira iwo kuzula ndi kupasula ndi kugwetsa, ndi kuononga ndi kusautsa; momwemo ndidzayang'anira iwo kumangitsa mudzi ndi kubzyala, ati Yehova.