Jeremiah 31:29 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Masiku amenewo anthu sadzanenanso kuti, ‘Makolo adya mphesa zosapsa, koma ana ndiye achita dziru.’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Masiku omwewo sadzanenanso, Atate adya mphesa zowawa, ndi mano a ana ayayamira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Mʼmasiku amenewo anthu sadzanenanso kuti, “Makolo adya mphesa zosapsa, koma mano a ana ndiye achita dziru.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Masiku omwewo sadzanenanso, Atate adya mphesa zowawa, ndi mano a ana ayayamira.