Jeremiah 31:30 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma munthu aliyense adzafa chifukwa cha machimo ake. Aliyense wodya mphesa zosapsa, ndi iye yemweyo amene adzachite dziru.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma yense adzafa chifukwa cha mphulupulu yake; yense amene adya mphesa zowawa, mano ake adzayayamira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mʼmalo wake, munthu aliyense adzafa chifukwa cha tchimo lake. Iye amene adzadye mphesa zosapsazo ndiye amene mano ake adzachite dziru.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma yense adzafa cifukwa ca mphulupulu yace; yense amene adya mphesa zowawa, mano ace adzayayamira.