Jeremiah 31:36 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngati zochitika zimenezi zilekeka, Ine ndili pomwepo, pamenepo ndiye fuko la Israele lidzathe, ndipo silidzakhalanso mtundu wa anthu pamaso panga mpaka muyaya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ngati malembawa achoka pamaso panga, ati Yehova, pamenepo mbeunso ya Israele idzaleka kukhala mtundu pamaso panga kunthawi zonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati zimenezi zilekeka pamaso panga, akutero Yehova, pamenepo padzakhala pamathero a fuko la Israeli pamaso panga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ngati malembawa acoka pamaso panga, ati Yehova, pamenepo mbeunso ya Israyeli idzaleka kukhala mtundu pamaso panga ku nthawi zonse.