Jeremiah 31:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Lidzafika tsiku pamene alonda a pa mapiri a Efuremu adzafuula kuti, ‘Tiyeni, tipite ku Ziyoni kwa Chauta, Mulungu wathu!’ ”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti lidzafika tsiku, limene alonda a pa mapiri a Efuremu adzafuula, Ukani inu, tikwere ku Ziyoni kwa Yehova Mulungu wathu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Lidzafika tsiku pamene alonda adzafuwula pa mapiri a Efereimu nati, ‘Tiyeni tipite ku Ziyoni, kwa Yehova Mulungu wathu.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti lidzafika tsiku, limene alonda a pa mapiri a Efraimu adzapfuula, Ukani inu, tikwere ku Ziyoni kwa Yehova Mulungu wathu.