Jeremiah 32:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pambuyo pake ndidatenga makalata anga a chipangano, ina yomata, m'mene munali mau onse a chipangano, ndi ina yosamata.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndinatenga kalata wogulira, wina wosindikizidwa, monga mwa lamulo ndi mwambo, ndi wina wovundukuka;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pambuyo pake ndinatenga makalata anga a pangano, imodzi yomatidwa mʼmene munali malamulo onse a panganolo ndi ina yosamatidwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndinatenga kalata wogulira, wina wosindikizidwa, monga mwa lamulo ndi mwambo, ndi wina wobvundukuka;