Jeremiah 32:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndithudi Chauta Wamphamvuzonse, Mulungu wa Israele, akutitu idzafika nthaŵi pamene anthu azidzagulanso nyumba, minda ndi mitengo ya mphesa m'dziko lino.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti Yehova wa makamu, Mulungu wa Israele atero: Nyumba ndi minda ndi minda yamphesa idzagulidwanso m'dziko muno.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti Yehova Wamphamvuzonse, Mulungu wa Israeli akuti: Anthu adzagulanso nyumba, minda ndi mitengo yamphesa mʼdziko lino.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti Yehova wa makamu, Mulungu wa Israyeli atero: Nyumba ndi minda ndi minda yamphesa idzagulidwanso m'dziko muno.