Jeremiah 32:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu ndi dzanja lanu lamphamvu kwambiri mudatulutsadi anthu anu Aisraele ku Ejipito pochita zizindikiro zozizwitsa ndi ntchito zododometsa zimene zidaopsa adani athu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo munatulutsa anthu anu Israele m'dziko la Ejipito ndi zizindikiro, ndi zodabwitsa, ndi dzanja lamphamvu, ndi mkono wotambasuka, ndi mantha ambiri;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munatulutsa Aisraeli mʼdziko la Igupto ndi dzanja lanu lamphamvu pochita zizindikiro zozizwitsa ndi zodabwitsa zimene zinaopseza adani anu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo munaturutsa anthu anu Israyeli m'dziko la Aigupto ndi zizindikiro, ndi zodabwitsa, ndi dzanja lamphamvu, ndi mkono wotambasuka, ndi mantha ambiri;