Jeremiah 32:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mudaŵapatsa dziko lino, limene mudalonjeza makolo ao molumbira, dziko lamwanaalirenji.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo munawapatsa iwo dziko ili, limene munalumbirira makolo ao kuti mudzawapatsa, dziko moyenda mkaka ndi uchi;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munawapatsa dziko lino limene munalonjeza mwalumbiro kulipereka kwa makolo awo, dziko loyenda mkaka ndi uchi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo munawapatsa iwo dziko ili, limene munalumbirira makolo ao kuti mudzawapatsa, dziko moyenda mkaka ndi uci;