Jeremiah 32:31 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Mzinda umenewu wakhala ukuutsa mkwiyo wanga ndi ukali wanga kuyambira nthaŵi imene adaumanga mpaka lero lino. Nchifukwa chake ndiyenera kuuchotsa pamaso panga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti mudzi uwu unali woutsa mkwiyo wanga ndi ukali wanga kuyambira tsiku lija anaumanga mpaka lero, kuti ndiuchotse pamaso panga;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kuyambira tsiku limene mzindawu unamangidwa mpaka lero, wakhala ukuwutsa mkwiyo wanga ndi ukali wanga. Nʼchifukwa chake ndiyenera kuwuchotsa pamaso panga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti mudzi uwu unali woutsa mkwiyo wanga ndi ukali wanga kuyambira tsiku lija anaumanga mpaka lero, kuti ndiucotse pamaso panga;