Jeremiah 32:34 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adaika mafano ao onyansa m'Nyumba imene imadziŵika ndi dzina langa, ndipo adaiipitsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma anaika zonyansa zao m'nyumba yotchedwa dzina langa, kuti aidetse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anayika mafano awo onyansa mʼnyumba imene imadziwika ndi dzina langa ndipo anayipitsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma anaika zonyansa zao m'nyumba yochedwa dzina langa, kuti aidetse.