Jeremiah 32:39 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidzaŵapatsa mtima umodzi ndi mkhalidwe umodzi, kotero kuti azidzandiwopa nthaŵi zonse. Motero iwowo ndi ana ao omwe, zinthu zidzaŵayendera bwino.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo ndidzawapatsa mtima umodzi ndi njira imodzi, kuti andiope Ine masiku onse; kuwachitira zabwino, ndi ana ao pambuyo pao;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndidzawapatsa mtima umodzi ndi khalidwe limodzi kotero kuti azidzandiopa nthawi zonse ndipo iwo pamodzi ndi zidzukulu zawo zinthu zidzawayendera bwino.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo ndidzawapatsa mtima umodzi ndi njira imodzi, kuti andiope Ine masiku onse; kuwacitira zabwino, ndi ana ao pambuyo pao;