Jeremiah 32:41 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidzakondwera kuŵachitira zabwino. Ndipo ndidzaŵakhazikitsa m'dziko lino mokhulupirika ndi mtima wanga wonse ndi kufuna kwanga konse.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Inde, ndidzasekerera iwo kuwachitira zabwino, ndipo ndidzawaoka ndithu m'dziko lino ndi mtima wanga wonse ndi moyo wanga wonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndidzakondwera powachitira zabwino, ndipo ndidzawakhazikitsa ndithu mʼdziko lino ndi mtima wanga wonse ndi moyo wanga wonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Inde, ndidzasekerera iwo kuwacitira zabwino, ndipo ndidzawaoka ndithu m'dziko lino ndi mtima wanga wonse ndi moyo wanga wonse.