Jeremiah 32:43 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu adzagulanso minda m'dziko lino limene inu mumati nlosiyidwa, lopanda munthu ndi nyama yomwe, chifukwa adalipereka kwa Ababiloni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo minda idzagulidwa m'dziko lino, limene muti, Ndilo bwinja, lopanda munthu kapena nyama; loperekedwa m'dzanja la Ababiloni.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Adzagulanso minda mʼdziko muno, limene inu mukuti, ‘Ndi dziko losiyidwa, lopanda anthu kapena nyama, pakuti linaperekedwa kwa Ababuloni.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo minda idzagulidwa m'dziko lino, limene muti, Ndilo bwinja, lopanda munthu kapena nyama; loperekedwa m'dzanja la Akasidi.