Jeremiah 32:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Hanamele, mwana wa Asalumu, amalume anga, akudzandiwona, ndipo adzandiwuza kuti, ‘Gula munda wanga wa ku Anatoti, poti iweyo ndiye woyenera kuuwombola.’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Taonani, Hanamele mwana wa Salumu mbale wa atate wako adzadza kwa iwe, kuti, Ugule munda wanga uli ku Anatoti; pakuti mphamvu yakuombola ndi yako kuugula.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Taonani, Hanameli mwana wa Salumu, amalume ako akubwera ndipo adzakuwuza kuti, ‘Gula munda wanga wa ku Anatoti, chifukwa iwe ndiwe mʼbale wanga ndipo ndiwe woyenera kuwuwombola.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Taonani, Hanameli mwana wa Salumu mbale wa atate wako adzadza kwa iwe, kuti, Ugule munda wanga uli ku Anatoti; pakuti mphamvu yakuombola ndi yako kuugula.