Jeremiah 32:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero ndidagula mundawo ku Anatoti kwa Hanamele msuweni wanga, ndipo mtengo wake unali masekeli asiliva 17.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndinagula mundawo wa ku Anatoti kwa Hanamele mwana wa mbale wa atate wanga, ndimyesera ndalama, masekeli khumi ndi asanu ndi awiri a siliva.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
choncho ndinagula munda wa ku Anatoti kwa Hanameli msuweni wanga, ndipo ndinamupatsa masekeli asiliva 17.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndinagula mundawo wa ku Anatoti kwa Hanameli mwana wa cibale wa atate wanga, ndimyesera ndalama, masekele khumi ndi asanu ndi awiri a siliva.