Jeremiah 33:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta adalankhulanso ndi Yeremiya kachiŵiri, akadali m'ndende m'bwalo la alonda a mfumu, adati,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mau a Yehova anadza kwa Yeremiya nthawi yachiwiri, pamene iye anali chitsekedwere m'bwalo la kaidi, kuti,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yeremiya akanali mʼndende mʼbwalo la alonda, Yehova anayankhula nayenso kachiwiri nati:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mau a Yehova anadza kwa Yeremiya nthawi yaciwiri, pamene iye anali citsekedwere m'bwalo la kaidi, kuti,