Jeremiah 33:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta akuti, “Anthu amanena za malo ano kuti ndi bwinja, opanda munthu ndi nyama yomwe. Komabe m'mizinda ya Yuda ndi m'miseu ya Yerusalemu m'mene tsopano muli zii, mopanda munthu ndi nyama yomwe, mudzamveka
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Atero Yehova: M'malo muno, m'mene muti, Ndi bwinja, mopanda munthu, mopanda nyama, m'midzi ya Yuda, m'makwalala a Yerusalemu, amene ali bwinja, opanda munthu, opanda wokhalamo, opanda nyama,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Yehova akuti, ‘Inu mumanena za malo ano kuti ndi bwinja,’ malo opandamo anthu kapena nyama. Komatu mizinda ya Yuda ndi mʼmisewu ya mu Yerusalemu mʼmene tsopano muli zii mudzamvekanso
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Atero Yehova: M'malo muno, m'mene muti, Ndi bwinja, mopanda munthu, mopanda nyama, m'midzi ya Yuda, m'makwalala a Yerusalemu, amene ali bwinja, opanda munthu, opanda wokhalamo, opanda nyama,