Jeremiah 33:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta Wamphamvuzonse akunena kuti, “Ku malo ano a chipululu opanda munthu ndi nyama yomwe, ndi ku mizinda yake yonse, kudzakhalanso mabusa kumene abusa angaŵetereko nkhosa zao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova wa makamu atero: M'malo muno, muli bwinja, mopanda munthu ndi nyama, m'midzi yake yonse, mudzakhalanso mokhalamo abusa ogonetsa zoweta zao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Yehova Wamphamvuzonse akuti, ‘Malo ano, a chipululu ndi wopanda anthu kapena nyama, mʼmizinda yake yonse mudzakhala msipu umene abusa adzadyetserako nkhosa zawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova wa makamu atero: M'malo muno, muli bwinja, mopanda munthu ndi nyama, m'midzi yace yonse, mudzakhalanso mokhalamo abusa ogonetsa zoweta zao.