Jeremiah 33:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta akutinso, “Akubwera masiku pamene ndidzachitadi zimene ndidalonjeza anthu a ku Israele ndi a ku Yuda.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Taonani, masiku alinkudza, ati Yehova, ndidzakhazikitsa mau abwino aja ndinanena za nyumba ya Israele ndi za nyumba ya Yuda.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Taonani masiku akubwera,’ akutero Yehova, ‘pamene ndidzachitadi zokoma zimene ndinalonjeza Aisraeli ndi nyumba ya Yuda.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Taonani, masiku alinkudza, ati Yehova, ndidzakhazikitsa mau abwino aja ndinanena za nyumba ya Israyeli ndi za nyumba ya Yuda.