Jeremiah 33:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zoonadi, Chauta akunena kuti, “Davide sadzasoŵa mdzukulu woloŵa m'malo mwake pa mpando waufumu wa Israele.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti Yehova atero: Davide sadzasowa munthu wokhala pa mpando wachifumu wa nyumba ya Israele;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova akunena kuti, ‘Davide sadzasowa mdzukulu wolowa mʼmalo mwake pa mpando waufumu wa Israeli,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti Yehova atero: Davide sadzasowa munthu wokhala pa mpando wacifumu wa nyumba ya Israyeli;