Jeremiah 33:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidzakhazikanso pabwino anthu a ku Yuda ndi a ku Israele, ndi kuŵabwezera momwe adaaliri poyamba.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndidzabweza undende wa Yuda ndi wa Israele, ndipo ndidzamangitsa mudzi wao, monga poyamba paja.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndidzawakhazikanso Ayuda ndi Aisraeli ku dziko lawo, ndipo ndidzawabwezera monga mmene analili poyamba.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndidzabweza undende wa Yuda ndi wa Israyeli, ndipo ndidzamangitsa mudzi wao, monga poyamba paja,