Jeremiah 34:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Chauta adauza Yeremiya kuti
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
chifukwa chake mau a Yehova anadza kwa Yeremiya kuchokera kwa Yehova, kuti,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono Yehova anawuza Yeremiya kuti:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
cifukwa cace mau a Yehova anadza kwa Yeremiya kucokera kwa Yehova, kuti,