Jeremiah 34:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
akalengeze kwa anthu mau a Chauta akuti, “Ndidachita chipangano ndi makolo anu pa tsiku limene ndidaŵatulutsa ku dziko la Ejipito ku nyumba ya ukapolo ija. Chipanganocho chidati:
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova Mulungu wa Israele atero: Ndinapangana mapangano ndi makolo anu tsiku lija ndinawatulutsa m'dziko la Ejipito, kutuluka m'nyumba ya ukapolo, kuti,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Yehova Mulungu wa Israeli akuti: Ine ndinachita pangano ndi makolo anu pamene ndinawatulutsa ku Igupto, mʼdziko la ukapolo. Ine ndinati,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova Mulungu wa Israyeli atero: Ndinapangana mapangano ndi makolo anu tsiku lija ndinawaturutsa m'dziko la Aigupto, kuturuka m'nyumba ya ukapolo, kuti,