Jeremiah 34:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amene ankadutsa pakati pa zigawo ziŵiriwo anali akulu a ku Yuda ndi a ku Yerusalemu, atsogoleri a boma, ansembe, ndiponso anthu a m'dzikomo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
akulu a Yuda, ndi akulu a Yerusalemu, adindo, ndi ansembe, ndi anthu onse a m'dziko, amene anapita pakati pa mbali za mwanawang'ombe;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Amene ankadutsa pakati pa zigawozo anali atsogoleri a Yuda ndi Yerusalemu, akuluakulu a bwalo, ansembe ndi anthu onse a mʼdzikomo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
akulu a Yuda, ndi akulu a Yerusalemu, adindo, ndi ansembe, ndi anthu onse a m'dziko, amene anapita pakati pa mbali za mwana wa ng'ombe;