Jeremiah 35:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pa nthaŵi imene Yehoyakimu, mwana wa Yosiya, anali mfumu ya ku Yuda, Chauta adalankhula nane ine Yeremiya. Adati,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mau amene anadza kwa Yeremiya kuchokera kwa Yehova masiku a Yehoyakimu mwana wa Yosiya, mfumu ya Yuda, kuti,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova anayankhula ndi Yeremiya nthawi ya ulamuliro wa Yehoyakimu mwana wa Yosiya mfumu ya Yuda, kuti:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mau amene anadza kwa Yeremiya kucokera kwa Yehova masiku a Yehoyakimu mwana wa Yosiya, mfumu ya Yuda, kuti,